Song Lyrics:
LYRICS
Song Title: Alonda
Artist:LUKI
Production: King Duda
VERSE 1
Tilila misozi lero
Kukuwa mwana wapita dzulo
Ka nyenyezi kaja
sikadzawalanso
Chimwemwe chija
Sitidzachimvanso
Ulumali chiphyinjo chodetsa nkhawa
Khunguli chifukwa cholanda moyo.
HOOK
Ife ndife ndi alonda
ndife alonda
tonse ndife alonda X3
VERSE 2
Mlonda wa mmbale wanga
Alubino
Akuyenda ndi mantha
Kuthawitsa moyo
Ngat ndiwe neba neba
Mmudzi mwathu ndife amodzi
Tikaima tonse pamodzi nkhanza titha kuzigonjetsa
Poti sa nasankhe kukhala osiyana nafe
Poti Sanasankhe chonde tisawataye
Iwo sanasankhe moyo tisawalande
Aahh eheh
HOOK
Ife ndife ndi alonda
ndife alonda
tonse ndife alonda X3
VERSE 3
Ife ndife alonda
Titenge mbali samala mmbale wathu chikondi dzoola
Ngati mafuta nyali tiwale tithandize anzathu kuona
Zoona
Ati ufuna dola
Nkhwilu ya chuma yaletsa kuona zoona
Mtima wanga ulila neh
Moyo wanzawotu zowona ayesa ndi golide
Koma afuwula bwanji akawandimva awopa mawa apita neh
Malawi bwanji
Waleka kuopa chauta ukukhetsa mwazi mwazi
Wathu ufanana
Wasambila mmanja ulendo wokafumbataaa
Tembenuka umuyang’ane
Kulichete akukuwabe
Udindo wathu tisamalane
From Chitipa to nsanje tonse
HOOK
Ife ndife ndi alonda
ndife alonda
tonse ndife alonda X3