{"id":313852,"created_at":"2024-09-07 00:29:44","updated_at":"2025-07-06 09:03:53","deleted_at":null,"published_at":"2024-09-07 00:29:44","original_id":null,"artist_id":153321,"title":"Akondwele","slug":"akondwele","status":"published","description":null,"album_id":null,"streets":1,"source_type":"s3","source":"file","lyrics":"Pamene anthu awili akukondana ma hater sangalephele (sangalephere)\r\nNdekuti ifeso mene tikukondana ma hater sangalephele\r\nChoncho afuna tisiyane afuna tisiyane\r\nKuti iwowo akondwele\r\nChoncho afuna tisiyane afuna tisiyane\r\nKuti iwowo akondwele\r\nKomabe komabe Usawamvele Seka makutu osamve zokamba zao\r\nKomabe komabe Usawamvele Seka makutu osamve\r\nChoncho afuna tisiyane afuna tisiyane\r\nKuti iwowo akondwele (iwowo akondwele)","download_count":41,"play_count":6,"restrict_download":0,"generated_thumbnail":null,"flag_count":0,"download_count_24":1,"download_count_24_at":"2025-07-06","reupload_sent":0,"thumb_path":"https:\/\/s3.eu-central-1.amazonaws.com\/sol-assets\/uploads\/public\/66d\/b82\/4cd\/thumb_1033760_300_300_0_0_crop.jpg","status_reason":"published","status_reason_alt":null,"tags":[]}
Song Lyrics:
Pamene anthu awili akukondana ma hater sangalephele (sangalephere)
Ndekuti ifeso mene tikukondana ma hater sangalephele
Choncho afuna tisiyane afuna tisiyane
Kuti iwowo akondwele
Choncho afuna tisiyane afuna tisiyane
Kuti iwowo akondwele
Komabe komabe Usawamvele Seka makutu osamve zokamba zao
Komabe komabe Usawamvele Seka makutu osamve
Choncho afuna tisiyane afuna tisiyane
Kuti iwowo akondwele (iwowo akondwele)
Subscribe to get the hottest exclusive music and content straight to your inbox!
Help us verify you before we continue...
We were not able to verify you. Please try again.