{"id":292033,"created_at":"2023-05-04 20:03:45","updated_at":"2025-04-17 23:39:09","deleted_at":null,"published_at":"2023-05-04 20:03:45","original_id":null,"artist_id":51568,"title":"Duwa (Feat. Hemon) Prod. by Jaguar Paws & Sir Odilo","slug":"duwa-feat-hemon-prod-by-jaguar-paws-sir-odilo","status":"published","description":null,"album_id":null,"streets":1,"source_type":"s3","source":"file","lyrics":"C.H.R.I.M \u2013 Duwa\r\n\r\nHook (Hemon):\r\n\r\nNdinagwada pansi kupemphelera iwe\r\nMkazi wangwiro wakumaloto \r\nYehova anayankha \r\nSiuyu wandipatsa langa duwa \r\nNdinagwada pansi \r\nkupemphelera iwe\r\nMkazi wangwiro wakumaloto \r\nYehova anayankha \r\nSiuyu wandipatsa langa duwa\r\n\r\nVerse 1(C.H.R.I.M): \r\nLove,\r\nWas complicated cause I kept chasing the wrong people\r\nThat's why my life changed when you came into the picture\r\nBeauty from ashes you made out of my heart wreckage\r\nYou brought summer into the winter\r\nAnd flipped the loss script\r\nSo, I had to make you my queen\r\nMwai subwera kawiri\r\nMphwemphwa ndi zambirimbiri\r\nZongokonda pamtendere ndiku darker ikapenga\r\nSingaphweketse chomwe wandipatsa namalenga\r\nNdipeza wina watenga nkusala ndekha pamvula\r\nMu den yopanda denga nde sendera ndikumajor \r\nSi zamovie komabe ndikhala wako director \r\nCoordinating this Divine written future together\r\nYou remain steadfast in the pain and hurdles\r\nEasy to love zi ma dinner date pa lake \r\nKomanso ku Nandos\r\nKonse ku park\r\nOkongola kunja ndi ngati\r\nWandipanikiza ndi chikondi cha khathi khathi \r\nThe starry skies, remain the witness\r\nSerenading Yah's approval of this communion\r\nAnd divorce is not an option\r\nWe ride till the wheels fall remains the notion\r\nThrough the sticks and stones \r\nThrough the peaks and lows\r\nYou my ride or die till Yeshua calls\r\nYeshua is King\r\n\r\nHook (Hemon):\r\n\r\nNdinagwada pansi kupemphelera iwe\r\nMkazi wangwiro wakumaloto \r\nYehova anayankha \r\nSiuyu wandipatsa langa duwa \r\nNdinagwada pansi \r\nkupemphelera iwe\r\nMkazi wangwiro wakumaloto \r\nYehova anayankha \r\nSiuyu wandipatsa langa duwa\r\nOoowohhhhh\r\nDuwaaaaa\r\nChokhumba cha Moyo wanga\r\nNdikuyamika ndalipeza langa duwa\r\nOoowohhhhh\r\nDuwaaaa\r\nChokhumba cha moyo wanga\r\nNdikuyamika\r\nNdalipeza langa duwa\r\n\r\nVerse 2 (C.H.R.I.M)\r\n\r\nTalk is cheap even when we use expensive mics\r\nBut am committed to our love and doing right\r\nIkapenga prayer the source for drawing all our might\r\nPatsogolo ndi Yeshua \r\nZa iweyo ndili shuwa\r\nNzeru zokhwima ngati tchuwa\r\nLove si chimatchini ngati swagga ya achina Vuwa\r\nSizopanana kukangana, kukakamizana \r\nWith you am home free ndipo itsanana\r\nNdiwe kadzuwa kuli m'dima unadzetsa masana \r\nKufewetsa gangster \r\nKudekhetsamo untchana \r\nYou all think about \r\nKupatulako Yeshua it's you I can't live without \r\nIf you tell the homies, \r\nI'll deny it \r\nI won't us to chart a course\r\nTake a vacation ku Chawe flex alittle and ride a horse\r\nI ain't wanna see you cause of me ukukhetsa misonzi\r\n\r\nBridge (Hemon):\r\nHeeyyyeaaahhh\r\nYehova wandipatsa umboni\r\nMwaiwe ndikondwera\r\nWakhazikika mu mtima mwangamu\r\nWakhazikika mu mtima \r\nMwangamu\r\n\r\nHook (Hemon):\r\n\r\nNdinagwada pansi kupemphelera iwe\r\nMkazi wangwiro wakumaloto \r\nYehova anayankha \r\nSiuyu wandipatsa langa duwa \r\nNdinagwada pansi \r\nkupemphelera iwe\r\nMkazi wangwiro wakumaloto \r\nYehova anayankha \r\nSiuyu wandipatsa langa duwa\r\nOoohhwwwooo\r\nDuwaaaaa\r\nChokhumba cha Moyo wanga\r\nNdikuyamika ndalipeza langa duwa\r\nOwhooooo\r\nDuwaaaa\r\nChokhumba cha moyo wanga\r\nNdikuyamika\r\nNdalipeza langa duwa\r\nDuwaaaa\r\nChokhumba cha moyo wanga\r\nNdikuyamika\r\nNdalipeza langa duwa\r\nOoowhhooo\r\nDuwaaaa\r\nChokhumba cha moyo wanga\r\nNdikuyamika\r\nNdalipeza langa duwa","download_count":110,"play_count":5,"restrict_download":0,"generated_thumbnail":null,"flag_count":0,"download_count_24":2,"download_count_24_at":"2025-04-17","reupload_sent":0,"thumb_path":"https:\/\/s3.eu-central-1.amazonaws.com\/sol-assets\/uploads\/public\/645\/3f3\/365\/thumb_945840_300_300_0_0_crop.jpg","status_reason":"published","status_reason_alt":null,"tags":[]}
Loading your song...
Downloads: 110
Song Lyrics:
C.H.R.I.M – Duwa
Hook (Hemon):
Ndinagwada pansi kupemphelera iwe
Mkazi wangwiro wakumaloto
Yehova anayankha
Siuyu wandipatsa langa duwa
Ndinagwada pansi
kupemphelera iwe
Mkazi wangwiro wakumaloto
Yehova anayankha
Siuyu wandipatsa langa duwa
Verse 1(C.H.R.I.M):
Love,
Was complicated cause I kept chasing the wrong people
That's why my life changed when you came into the picture
Beauty from ashes you made out of my heart wreckage
You brought summer into the winter
And flipped the loss script
So, I had to make you my queen
Mwai subwera kawiri
Mphwemphwa ndi zambirimbiri
Zongokonda pamtendere ndiku darker ikapenga
Singaphweketse chomwe wandipatsa namalenga
Ndipeza wina watenga nkusala ndekha pamvula
Mu den yopanda denga nde sendera ndikumajor
Si zamovie komabe ndikhala wako director
Coordinating this Divine written future together
You remain steadfast in the pain and hurdles
Easy to love zi ma dinner date pa lake
Komanso ku Nandos
Konse ku park
Okongola kunja ndi ngati
Wandipanikiza ndi chikondi cha khathi khathi
The starry skies, remain the witness
Serenading Yah's approval of this communion
And divorce is not an option
We ride till the wheels fall remains the notion
Through the sticks and stones
Through the peaks and lows
You my ride or die till Yeshua calls
Yeshua is King
Hook (Hemon):
Ndinagwada pansi kupemphelera iwe
Mkazi wangwiro wakumaloto
Yehova anayankha
Siuyu wandipatsa langa duwa
Ndinagwada pansi
kupemphelera iwe
Mkazi wangwiro wakumaloto
Yehova anayankha
Siuyu wandipatsa langa duwa
Ooowohhhhh
Duwaaaaa
Chokhumba cha Moyo wanga
Ndikuyamika ndalipeza langa duwa
Ooowohhhhh
Duwaaaa
Chokhumba cha moyo wanga
Ndikuyamika
Ndalipeza langa duwa
Verse 2 (C.H.R.I.M)
Talk is cheap even when we use expensive mics
But am committed to our love and doing right
Ikapenga prayer the source for drawing all our might
Patsogolo ndi Yeshua
Za iweyo ndili shuwa
Nzeru zokhwima ngati tchuwa
Love si chimatchini ngati swagga ya achina Vuwa
Sizopanana kukangana, kukakamizana
With you am home free ndipo itsanana
Ndiwe kadzuwa kuli m'dima unadzetsa masana
Kufewetsa gangster
Kudekhetsamo untchana
You all think about
Kupatulako Yeshua it's you I can't live without
If you tell the homies,
I'll deny it
I won't us to chart a course
Take a vacation ku Chawe flex alittle and ride a horse
I ain't wanna see you cause of me ukukhetsa misonzi
Bridge (Hemon):
Heeyyyeaaahhh
Yehova wandipatsa umboni
Mwaiwe ndikondwera
Wakhazikika mu mtima mwangamu
Wakhazikika mu mtima
Mwangamu
Hook (Hemon):
Ndinagwada pansi kupemphelera iwe
Mkazi wangwiro wakumaloto
Yehova anayankha
Siuyu wandipatsa langa duwa
Ndinagwada pansi
kupemphelera iwe
Mkazi wangwiro wakumaloto
Yehova anayankha
Siuyu wandipatsa langa duwa
Ooohhwwwooo
Duwaaaaa
Chokhumba cha Moyo wanga
Ndikuyamika ndalipeza langa duwa
Owhooooo
Duwaaaa
Chokhumba cha moyo wanga
Ndikuyamika
Ndalipeza langa duwa
Duwaaaa
Chokhumba cha moyo wanga
Ndikuyamika
Ndalipeza langa duwa
Ooowhhooo
Duwaaaa
Chokhumba cha moyo wanga
Ndikuyamika
Ndalipeza langa duwa
Subscribe to get the hottest exclusive music and content straight to your inbox!
Help us verify you before we continue...
We were not able to verify you. Please try again.