{"id":284544,"created_at":"2023-01-20 07:14:00","updated_at":"2025-07-01 13:15:58","deleted_at":null,"published_at":"2023-01-20 07:14:00","original_id":null,"artist_id":126980,"title":"Tili M'momo (Prod by Blxck Fyxh)","slug":"tili-mmomo-prod-by-blxck-fyxh","status":"published","description":null,"album_id":null,"streets":1,"source_type":"s3","source":"file","lyrics":"INTRO\r\n[beat playing]\r\n\r\n[VERSE I]\r\nAmangoyesa adzitiwona tukanda ya\r\nKumangoyesa adzitiwona tulira ya ya\r\nKoma sakuvetsa abalalika\r\nKunditchela ndale koma i'm standing feet ya\r\nKutseka makomo akudabwabe tili m'momo tili m'momo \r\nTikhala panja bwanji nkati muthoka za dolla ya \r\nTikhala panja bwanji nkati muthoka zo baller ya\r\nNgati umayesa uziwina wekha ukunama ukunama ukunama\r\nYe mfana wamakani wangobwela mwa ukali \r\nNafe mfuna dolla\r\nNafe tiveke kutali yaa \r\nNgati uthoka za dolla utipeza m'momo \r\nUthoka zowina utipeza m'momo\r\nUthoka zo scorra utipeza m'momo \r\nUthoka zoballer utipeza m'momo\r\n\r\n[HOOK]\r\nTili mmomo tili m'momo\r\nTili m'momo ya \r\nTungobwela mwa ukali situwopa \r\nSunandilenge ndiwe nafe tikuballer\r\nTili m'momo tili m'momo \r\nTili m'momo ya \r\nTungobwela mwa ukali situwopa\r\nSunandilenge ndiwe nafe tikuballer\r\nTili m'momo tili m'momo\r\nTili m'momo ya\r\nTili m'momo tili m'momo\r\nTili m'momo ya \r\n\r\n[VERSE II]\r\nTili m'momo aseh \r\nKusaka zi ndalama\r\nSitugona i swear\r\nAkufuna kundilasa angophonya onsewa\u00a0 angophonya onsewa\r\nAmakodwa adzatiwona tikulira \r\nSamafuna adzitiwona tikukodwa \r\nAmakodwa adzatiwona tikulira\r\nSamafuna adzitiwona tikunjoya \r\nKoma i'm sorry sunandilenge ndiwe aseh \r\nUkamango hater dzingoseka HAHAHA\r\nSundufowoka ndungovaya vuuu vuu mm\r\nUkamango hater dzingoseka HA HA HA\r\nSundufowoka ndungovaya vuuu vuu mmmm\r\n\r\n[HOOK]\r\nTili m'momo tili m'momo\r\nTili m'momo ya \r\nTungobwela mwa ukali situwopa \r\nSunandilenge ndiwe nafe tikuballer\r\nTili m'momo tili m'momo \r\nTili m'momo ya \r\nTungobwela mwa ukali situwopa\r\nSunandilenge ndiwe nafe tikuballer\r\nTili m'momo tili m'momo\r\nTili m'momo ya\r\nTili m'momo tili m'momo\r\nTili m'momo ya \r\n\r\n[OUTRO]\r\nEeh i'm sorry sunandilenge ndiwe aseh [Ndiwe aseh]\r\nNafe tikuwina tikudyela [Tikudyela]\r\nNafe tiku baller tiku scorra [Tiku scorra]\r\nNafe tikudyela tili m'momo tili m'momo [Tili m'momo ya Kiid ef]","download_count":112,"play_count":8,"restrict_download":0,"generated_thumbnail":null,"flag_count":0,"download_count_24":1,"download_count_24_at":"2025-07-01","reupload_sent":0,"thumb_path":"https:\/\/s3.eu-central-1.amazonaws.com\/sol-assets\/uploads\/public\/63c\/a22\/f0c\/thumb_919311_300_300_0_0_crop.jpg","status_reason":"published","status_reason_alt":null,"tags":[]}
Loading your song...
Downloads: 112
Song Lyrics:
INTRO
[beat playing]
[VERSE I]
Amangoyesa adzitiwona tukanda ya
Kumangoyesa adzitiwona tulira ya ya
Koma sakuvetsa abalalika
Kunditchela ndale koma i'm standing feet ya
Kutseka makomo akudabwabe tili m'momo tili m'momo
Tikhala panja bwanji nkati muthoka za dolla ya
Tikhala panja bwanji nkati muthoka zo baller ya
Ngati umayesa uziwina wekha ukunama ukunama ukunama
Ye mfana wamakani wangobwela mwa ukali
Nafe mfuna dolla
Nafe tiveke kutali yaa
Ngati uthoka za dolla utipeza m'momo
Uthoka zowina utipeza m'momo
Uthoka zo scorra utipeza m'momo
Uthoka zoballer utipeza m'momo
[HOOK]
Tili mmomo tili m'momo
Tili m'momo ya
Tungobwela mwa ukali situwopa
Sunandilenge ndiwe nafe tikuballer
Tili m'momo tili m'momo
Tili m'momo ya
Tungobwela mwa ukali situwopa
Sunandilenge ndiwe nafe tikuballer
Tili m'momo tili m'momo
Tili m'momo ya
Tili m'momo tili m'momo
Tili m'momo ya
[VERSE II]
Tili m'momo aseh
Kusaka zi ndalama
Situgona i swear
Akufuna kundilasa angophonya onsewa angophonya onsewa
Amakodwa adzatiwona tikulira
Samafuna adzitiwona tikukodwa
Amakodwa adzatiwona tikulira
Samafuna adzitiwona tikunjoya
Koma i'm sorry sunandilenge ndiwe aseh
Ukamango hater dzingoseka HAHAHA
Sundufowoka ndungovaya vuuu vuu mm
Ukamango hater dzingoseka HA HA HA
Sundufowoka ndungovaya vuuu vuu mmmm
[HOOK]
Tili m'momo tili m'momo
Tili m'momo ya
Tungobwela mwa ukali situwopa
Sunandilenge ndiwe nafe tikuballer
Tili m'momo tili m'momo
Tili m'momo ya
Tungobwela mwa ukali situwopa
Sunandilenge ndiwe nafe tikuballer
Tili m'momo tili m'momo
Tili m'momo ya
Tili m'momo tili m'momo
Tili m'momo ya
[OUTRO]
Eeh i'm sorry sunandilenge ndiwe aseh [Ndiwe aseh]
Nafe tikuwina tikudyela [Tikudyela]
Nafe tiku baller tiku scorra [Tiku scorra]
Nafe tikudyela tili m'momo tili m'momo [Tili m'momo ya Kiid ef]
Subscribe to get the hottest exclusive music and content straight to your inbox!
Help us verify you before we continue...
We were not able to verify you. Please try again.